For sales enquiries contact:
aubreymwale12@gmail.com

Benefits

Overall, ECO System helps Customers to reduce TCO (Total Cost of Ownership) costs and offers environmental friendly benefits.

Reduces fuel consumption:
10% – 30%

Amachepetsa kugwiritsa ntchito mafuta ochuluka

10% – 30%

Reduces maintenance costs:
DFP Filter, injectors, engine, EGR, catalytic converter etc.

Amachepetsa kukonza konza.

Kusintha Oil ndi fuel filters, ma injectors ndi mabvuto amu Engine

Reduces emissions:
70% – 90% (immediate and visible)

Amachepetsa Utsi kapena mpweya ochoka mu engine.

70% – 90 % (Pompo pompo utsi umatheratu)

Provides complete fuel burn, which results in increased horsepower

Imathandizira kugwiritsa ntchito mafuta onse omwe mwathira ndikuthandiziranso kuti Engine izikoka ndi mphanvu

Cost-effective: pay back cost of the unit within months

Njira yopindulitsa yotsika mtengo yopulumutsa mtengo ndi ndalama zolipira m’miyezi yochepa

ECO unit typical installation time is just 15 – 30 minutes

Kayikidwe ka chipangizochi mkosavuta mu mphindi 15- 30 umakhala wamaliza kumangilira